Mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF) Atupele Muluzi tsopano ali ndi tsamba la padera la mchezo wa pa Whatsapp.
Malinga ndi Muluzi, cholinga cha tsambali ndi kufuna kulumikizana mosavuta ndi anthu mdziko muno.
Pa tsambali mwa zina, Muluzi wati adziligwiritsa ntchito polumikizana ndi anthu mdziko muno pa nkhani zosiyana siyana.