chibvomelezifm
  • Home
  • Featured
  • Politics
  • Business
  • Entertainment
  • Lifestyle
  • Sports
  • About Us
  • Contact
  • Login
  • chibvomelezifm

    SULOM yapereka zifukwa zokwezera mtengo wa masewero

    Boma lati lilemba ogwira ntchito za umoyo mdziko muno

    Apolisi ati asintha kagwiridwe ka ntchito

    SULOM yapereka zifukwa zokwezera mtengo wa masewero

    Blessings MeloApril 4, 20250100 views

    Bungwe loyendetsa masewero a mpira wa miyendo a mu mpikisano wa Super League la SULOM lafotokoza chifukwa chomwe chachititsa kuti likweze mulingo…

    Read more

    Boma lati lilemba ogwira ntchito za umoyo mdziko muno

    Blessings MeloApril 4, 2025099 views

    Boma lati lilemba ntchito ogwira ntchito za umoyo owonjezera mdziko muno. Wafotokoza izi ndi nduna ya za umoyo Khumbize Kandondo Chiponda, pomwe…

    Read more

    Apolisi ati asintha kagwiridwe ka ntchito

    Blessings MeloApril 4, 20250102 views

    Mkulu wa a polisi mdziko muno Merlyn Yolamu walonjeza kuti awonetsetsa kuti a polisi akugwira ntchito zawo motsatira malamulo, pothana ndi mchitidwe…

    Read more

    Olemba nkhani aziteteze pa nthawi yazipolowe

    Blessings MeloApril 4, 2025087 views

    Atola nkhani mdziko muno awapempha kuti ateteze moyo wao pa nthawi yomwe akutola ndi kulemba nkhani zokhudza zipolowe. Langizoli laperekedwa pa maphunziro…

    Read more

    Chipani cha People’s Development PDP chasintha tsiku la zisankho zachipulula

    Blessings MeloApril 3, 20250104 views

    Chipani cha People’s Development-PDP chalimbikitsa zokonzekera zake za ntchito yosankha odzachiyimira pa mipando ya aphungu a ku nyumba ya Malamulo pa chisankho…

    Read more

    Timu ya Silver Strikers yalora kusewera masewero ake pa bwalo la Bingu

    Blessings MeloApril 3, 2025097 views

    Kusamvana komwe kunalipo pakati pa bungwe loyendetsa masewero a mpira a mu mpikisano wa Super League, la SULOM ndi timu ya Silver…

    Read more

    Timu ya Scorchers ithambitsana ndi Banyana-Banyana la mdziko la South Africa

    Blessings MeloApril 3, 20250105 views

    Timu ya mpira wa miyendo yomwe osewera ake ndi atsikana yalimbikitsa zokonzekera zake za masewero awiri a pa ubale ndi timu ya…

    Read more

    Higher education students loan yotsekula nyengo yopereka ndalama zolipilira ophunzira msukulu za mdziko muno

    Blessings MeloApril 3, 20250123 views

    Ophunzira a msukulu za ukachenjede omwe sangathe kudzilipilira okha ndalama za maphunziro awo tsopano ali ndi mwai olandira thandizoli kuchokera ku bungwe…

    Read more

    MULUZI AKHAZIKITSA TSAMBA LA MCHEZO

    Blessings MeloApril 2, 2025083 views

    Mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF) Atupele Muluzi tsopano ali ndi tsamba la padera la mchezo wa pa Whatsapp. Malinga…

    Read more

    Muluzi wakhazikitsa tsamba la mchezo

    Blessings MeloApril 1, 2025072 views

    Mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF) Atupele Muluzi tsopano ali ndi tsamba la padera la mchezo wa pa Whatsapp. Malinga…

    Read more

    Posts navigation

    1 2
    View Desktop Version

    Powered by PenciDesign

    Back To Top