ODWALA PA CHIPATALA CHA NGABU SAKULANDIRA CHAKUDYA KWA CHAKA TSOPANO.
Patha pafupifupi chaka odwala omwe agonekedwa pa chipatala cha Ngabu asakulandira chakudya chilichonse chophikidwa pa chipatalachi, popanda chifukwa chodziwika bwino.…