Achinyamata a kukatula kalata ya madandaulo pa za zaka zomwe munthu angathe kuyima ngati mtsogoleri wadziko
Zokonzekera zafika kumapeto mu mzinda wa Lilongwe za zionetsero zokwiya ndi kuchedwa kwa nyumba ya malamulo kukambirana nkhani yokhudza mulingo wa zaka…