Bungwe loyendetsa masewero a mpira wa miyendo a mu mpikisano wa Super League la SULOM lafotokoza chifukwa chomwe chachititsa kuti likweze mulingo …
April 2025
-
-
Boma lati lilemba ntchito ogwira ntchito za umoyo owonjezera mdziko muno. Wafotokoza izi ndi nduna ya za umoyo Khumbize Kandondo Chiponda, pomwe …
-
Mkulu wa a polisi mdziko muno Merlyn Yolamu walonjeza kuti awonetsetsa kuti a polisi akugwira ntchito zawo motsatira malamulo, pothana ndi mchitidwe …
-
Atola nkhani mdziko muno awapempha kuti ateteze moyo wao pa nthawi yomwe akutola ndi kulemba nkhani zokhudza zipolowe. Langizoli laperekedwa pa maphunziro …
-
Chipani cha People’s Development-PDP chalimbikitsa zokonzekera zake za ntchito yosankha odzachiyimira pa mipando ya aphungu a ku nyumba ya Malamulo pa chisankho …
-
Kusamvana komwe kunalipo pakati pa bungwe loyendetsa masewero a mpira a mu mpikisano wa Super League, la SULOM ndi timu ya Silver …
-
Timu ya mpira wa miyendo yomwe osewera ake ndi atsikana yalimbikitsa zokonzekera zake za masewero awiri a pa ubale ndi timu ya …
-
Uncategorized
Higher education students loan yotsekula nyengo yopereka ndalama zolipilira ophunzira msukulu za mdziko muno
Ophunzira a msukulu za ukachenjede omwe sangathe kudzilipilira okha ndalama za maphunziro awo tsopano ali ndi mwai olandira thandizoli kuchokera ku bungwe …
-
Mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF) Atupele Muluzi tsopano ali ndi tsamba la padera la mchezo wa pa Whatsapp. Malinga …
-
Mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF) Atupele Muluzi tsopano ali ndi tsamba la padera la mchezo wa pa Whatsapp. Malinga …